Kwachitika zochitisa chidwi pamene ma twins amene anabadwa ndi thupi lophatana, mmodzi wakwatila.
Ma twins wa omwe anabadwa chaka cha 2001 mu dziko la Mexico, ndi anthu amene anabadwa modabwitsa kwambiri pakuti ndi ophatana ziwalo. Aliyense ali ndi mikono yake koma zidali zawo ndi nsana ndi zophatana. Kotelo aliyense ali ndi mwendo umodzi, wina waku manja pamene wina waku mmazele.
Atsikanawa omwe maina awo ndi Carmen komanso Lupita, azaumoyo ankati sangakhale moyo kwa masiku oposa atatu atabadwa, koma Mulungu ndi wamkulu tikunena pano mpaka akwana dzaka 24.
Tsopano chomwe chachititsa chidwi anthu ndi chakuti, mmodzi mwa atsikana wa yemwe dzina lake ndi Carmen wapeza mamuna ndipo wakwatiwa, pamene twin sister wake Lupita iyeyo akuti ali single ndipo zokwatila sakuzifuna. Zikuoneka kuti ngakhale anthuwa ali ophatana ziwalo koma aliyense amapanga zake, ngakhale kuti chilichonse amapangila limodzi.
Mwachisanzo "Lupita" anadandaula kuti kukwatila kwa sister wakeyo kukumapangisa kuti azionelela sister wake yu akamagonana ndi mamuna wake, pamene iyeyo ali single. Mwina kutsogoloku nayeso atha kupeza mamuna wake koma tikunena pano ukwati wa sister wake wachitika kale ndipo umu ndi mmene ma picture a ukwati amaonekela.
ZODABWISA
Interesting
Eeeh ok
Bola moyo
Congratulations to the new couple
Ok bola
Allah salakwisa
Zodwabwitsa
Wonderful
Kodi aliyense ali ndi pake pake kapena malo nda modzi
God's plan always the best
Nde aaaaa🙄🙄🙄🙄
That's nice congratulations
Nde mwat pogonanapo zumakhala bwanji 😠kpn ali ndipawili?
Angokambilana avane mamuna akhale modziyo basi
Cheating yosalesdwa
Nde kuti aliyense Ali ndi Malo ake ake
Zosangalatsa kwambiri
Moyo🤔🙌
Mulungu alemekezeke
Nde wina wa single yo amamva bwanj nzakeyo akamagogona?
Zozizwitsa ku mwamba kulemekezeke
Power of God only
Power of God only
Power of God only
Koma ndiye zoopsatu
Km ndiye zidabwisatu
Hy
Km ndiye azikhala bwanji cz onsewo ndi thupi limodzi
Mmmm Mulungu ngodabwisa
Angokwatira onsewo basi
That means both of them have one vargina
Kodi Ali ndi ma private parts two or one private part???
Sono azionelela bwanji ? Mesa maliseche awo ndi amodzi?
Nde tizit aliense alinso ndi vargina Yake Yake or how Ndichotsen umbuli🙄
Nde tizit aliense alinso ndi vargina Yake Yake or how Ndichotsen umbuli🙄
Izitu nde zoopsa🙄🙄🙄
Koma mesa azimvabe nawo zokhuza kugonanakozo and izo wangoyakhula chifukwa mesa Ali ndi chiwalo chimoz chofunisa mamunacho koma mmh ndzovuta kukamba kwake
Mwamuna yo chiripo chomwe akutsata coz sizoona
Nde mmhuu, kodi ndifunse bwanji I e pamenepa? Akamafuna kupita ku toilet amapita onse?
Iiiiiii koma nde zovutatu abale moti akumamuonelanso mlamu wakeyo😳
Langa ndifusobe sindikunvetsa, mukuti ndiophathana, zomwe zikutathauza kuti maliseche awo ndamodzi? Kapena ndiosiyana?
Winayo ndikwatila ine adekhe kkkk