Article
Kanye west wasinthanso dzina lake, kuchoka ku 'Ye'. Akuti pa zifukwa izi:

Kanye west wasinthanso dzina lake, kuchoka ku 'Ye'. Akuti pa zifukwa izi:

Kanye 'Ye' West walengeza kuti wasinthanso dzina lake

Akuti sizomutchulanso kuti 'Ye' akuti dzina limenelo so ayi, panopa wabwela ndi dzina lina lomwe akufuna kuti aliyense azimutchulira. Anthu adabwa naye oimba wa dzaka 48 yu kuti Kodi iyeyu kwenikweni akufuna chani?

Pakatipa anagundika kunyoza anthu, komanso mitindu ya zi khalidwe zosiyana ndiye pofuna kuonesa kuti basi zonyoza anthu zo sazapangaso ndipo wabadwa mwatsopano wangoganiziza zosithanso dzina lake. Moti tikunena pano ma contract ake a business wayamba kale kugwilitsa ntchito dzina la tsopano li.

Koma Funso kumati, Kodi dzina la tsopano lo ndi lokuti chani?

Aka khala kachiwili mkulu yu kuzisintha dzina, mu chaka cha 2021 anasintha dzina kukhala "Ye" kuchokela ku Kanye West. Tsopano pano akuti iyeyu akufuna azitchulidwa kuti "Ye Ye"

Admin Jeffrey

Comment Below

upload your music with us to get maximum reach out!