Article
Ndichufukwa chani akuti pali 3% chance kuti Yesu atha kubwela chaka chomwe chino?

Ndichufukwa chani akuti pali 3% chance kuti Yesu atha kubwela chaka chomwe chino?

PA internet anthu ayamba kubetchelana ndalama pa nkhani yokuti "Yesu atha kubwela chaka chino chisanathe" .

Kutengela mmene dziko likuyendela company yi yomwe imapanga mipikisano yolosela (prediction market) yamvesedwa kuti osata malemba ena akuti zizindikilo za kubwela kwa Yesu zachitika, ndipo ndizotheka ndithu kuti atha kutulukila chaka cha 2025 chisanathe.

Kotelo iwowa monga mwa nthawi zonse amapanga mipikisano yolosela zisankho komaso ma stock market, aika pa msika kuti anthu abetche kuti ngati akukhulupilira za nkhani yi kapena ayi.

Tikunena pano apeleka ma odds okwana 3%, ndipo ndalama zakwana K80 million kwa omwe angalosele kuti abwela di, mtengo wu ukhala ukukwela ena akamaloselaso pa PolyMarket po.

Pamene akulu akulu a mpingo aweluza company yi kuti izingopanga zolosela zisankho zomwe zo koma izizi azisiye, chifukwa akuchitazo ndi kuba. Nanga olo munthu awine ndalama zo koma Yesu atabwela, akazidyela kuti pakuti dziko li zakhala latha. Pamene ena akuti Palibe vuto kwenikweni pa nkhani yi, Inu Mukuonapo bwanji?

Mukuona kuti ndiyoyenela kumapanga maloselo ngati amene wawa?

Admin Jeffrey

Comment Below

12 Comments

Vincent Neva

Yesu sakubwela pano ay

Topola palipose

Ndimakape pajatu yesu azafika Ngati mbala 😏

Dael sidess

Let's just watch n see ... God knows.,.

Micah kandiyanja

Tsiku lobwel yesu palibe amalidziwa kmaso palibe adzalidzi chifkwa bible limati adzafika ngt mbala pamaso pathu

Micah kandiyanja

Tsiku lobwel yesu palibe amalidziwa kmaso palibe adzalidzi chifkwa bible limati adzafika ngt mbala pamaso pathu

Aubrey Kausiwa

Jesus can't come this year

Dixon Lendson

Yesu adzabwera kma tsiku silimadziwika choncho kuti Chaka Chino ndibodza

David Chonde

Yesu akubwera koma palibeakuziwa za nthawi

ARSHER

Izi zolakwika and we don't need to make bet with the word of God

Mphatso ntonyo

Yesu akubwera

Dann January

Eeeh 🙄

bs

zooona izi?

upload your music with us to get maximum reach out!