M'zimayi amene anafa wadzuka mu bokosi, akufuna kumukwilira.
Mayiyu amene ndi wa dzaka 88 zakubadwa, anasala pang'ono kuti amuike mmanda pamene anazizimuka. Izi zadabwitsa anthu ambili ku dziko la Czech Republic ndipo vuto lalikulu akuti anali akuchipatala amene analengeza kuti mayiyu wamwalira koma asanamulabadile bwinobwino.
Amuna wo a mayiwa akuti zonse zi zinayamba pamene anadzuka mamawa ndikuona kuti akazawo sakupeza bwino, koma atafika ku chipatala anangofikila kuwauuza kuti akazawo amwalira ngakhale a chipatala wo sanachite nawo chidwi kwenikweni.
Mpaka kukafika kosambisa maliro osadziwabe kuti munthu ali moyo, kufikila kuika thupi lawo mu bokosi ndi pamene amazizimuka (ma bokosi omwe amatsegula nkhope kumaoneka aja)
Apolisi tikunena pano ayambapo kafukufuku kwa ogwila ntchito ku chipatala chi pokanika kupeleka chisamaliro choyenela komanso pogwila ntchito mosazipeleka, akuti ndikutheka anthu ambili amatha ku walengeza kuti amwalira koma ali moyo ndiye ndi koyenela kupanga po kanthu.
Tikunena pano mayiyo ali ku chipatala chomwecho ndipo a kulandilano thandizo, ndipo ma report akuonetsa kuti akhala di bwino ndithu.
Zovuta, zinakakhala ku Malawi bwenzi patalowa kale zikhulupiliro apa.
Source of news: the daily mail
Zosachitilaso mwina umkuva kaitaneni azamba🤣🤣🤣🤣🤣
Kunoko kumalawi nde kut mayiwo ndi mfiti 🤣🤣🤣
Uyu Basitu wapulumuka
Ku Malawi ukhala ufiti😭😂😂😂
Kunakakhala ku Malawi kuno akanangomalizitsa sure 🙌
Mmmm zovuta kwambiri
Kuli Ku Ku Africa kuno akanawakong'ontha kuwamalidxitsa
Zovutat kobasi
Zimachitika
Ambiri amafelad m'bokosi akakwililidwa
We are protected to God
It's not yet for her
Nthawi yake sinakwane,
Nthawi yoti afe sinakwane alimbikile kupemphera
Nthawi yoti afe sinakwane alimbikile kupemphera
Ndipo ku Malawi sitizatheka
Eeh achipatala pulizi
Sometimes people they are die but God sent them back to repent. Sure
Achipatala masiku ano akumanyada kwambir akumakhala ngat sazamwalira
Zonvuta mmmh
Achipatala pena matiyikitsa a2 amoyo2 🙄
Zovutatu mmhu
Kuli khmalawi uva ndi ufiti🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Zimachitika
Yangadyedatu pele
Zosakhala bwino 🤔🤔🤔
Zosakhala bwino
Izi si zachilendo.
Eeèeee iyiyi kma ndiyina yake
Nkhan ngat izizi ndizovuta kuweluza kwake, nanga mpaka kukasambisa munthu osazuka kukadzuka nthawi yoona nkhope, let God judge
Zosakhala bwino😥 atadyatu angapotu awa mkumat athelako pomwe zisali chomcho
Tsiku lawo laifa silinakwane,Allah alinawo cholinga
Zovuta 😌
Zovutatu
Anachita bwino kuzuka mwa changu adakangochedwa pang'ono bwez atadzukira Ali Pasi mkufa imfa yowawa
Zinthu zake🙌
Moyo unazaza ndi zinyengo ,,, nthawi yake sinakwane Mulunguysanafune🙏🙏
A Chipatala akatero adali busy pa tiktok
Yemwe ananena kuti mayiwo amwalira koma osamulabadira akuyenera kukayakha mlandu.
A police akuyenera kupeleka chirango kwa munthu amene adalengeza kuti mayiyu wamwalira kuti anzake opanga zotelewa atendelepo mphunziro.