Article
Ibrahim Traore wakaniza  Burna Boy kupangitsa show yaulere ku Burkina Faso, mwamanyazi.

Ibrahim Traore wakaniza Burna Boy kupangitsa show yaulere ku Burkina Faso, mwamanyazi.

Masamba a mchezo wakula msunso pamene president Ibrahim Traore wakaniza oimba Burna Boy kupangitsa show yaulere ku Burkina Faso, mwamanyazi.

Masiku a m'mbuyomo oimba waku Nigeria Burna Boy analengeza komanso kupempha kuti akufuna atapangitsa show ya ulere mu dziko la Burkina Faso, ngati njila imodzi yoyamikila mmene dziko li likuyendela pa utsogoleri wa a Ibrahim Traore.

Zachisoni kwamvekano ma report okuti a Traore akana zimenezi, ndipo iwo anena kuti pakadali pano dziko lawo lili busy ndi zitukuko za serious ndiye zama show zi kwa iwo akungoona ngati ndi zinthu zongopeleka chitsokonezo m'dziko Kotele sakuifuna mphatso yi.

Kayankhidwe ka a Traore ambili akatenga ngati kochititsa manyazi kwa oimba yu ndipo mpaka munuwake Burna Boy wayankhulaponso kale kuti iye popeleka show yaulere kunali kuonesa ulemu chabe kwa anthu aku Africa, samachita izi pofuna kuonesa chipogwe chilichonse.

Burna Boy wapitiliza kunena kuti kwa iyeyo nyimbo ndi chinthu Chimodzi chomwe chimabweletsa anthu pa modzi komanso nsangulutso, kotelo iyeyu wasutsa kuti nyimbo zimapeleka chitsokonezo pa zitukuko za serious ngati mmene anenela a Traore.

Mwachidule tingoti zalowa beef, Inu Mukuona kuti akunena zoona pamene ndi ndani? A Traore achita bwino ku kana show ya ulere yi pa zifukwa akambazi?

Nanga burna Boy kunali koyenela kunena kuti apeleke show ya ulere ku dziko la Burkina Faso?

Admin Jeffrey

Comment Below

71 Comments

2025

2025

2026

2025

2026

2025

2025

2026

2026

2025

2026

2025

2025

2025

2025

2026

2025

2025

2026

2026

2025

2025

2026

2025

2026

2026

2025

2026

2025

2025

2026

2026

2025

BN

KKKKK

madalitso shan

zaci soni

madalitso shan

zaci soni

Omj

Wachita bwno traero kudula pangano la show yaulere , in case outside intruders can find a chance to attach Traero while his bus with fuck events denie it it's okay , viva African God bless Giant Hero Traero

Ngwaz Vybz Jickenz

Kaya zawo izoooo kkkk

Generous Kapinga

Za show sizingapereke phindu ku dzikolli

Ek

The boy has to leave the way it is

Chikondi

Wachita bho kukana

Jamie

Nkhan ndiyokhudza zinthu mom we zilili kumeneko, I mean akuteteza Dziko kuziwembu

Gorge

Aliyse kumbali yake akuyankhula momwe wayimvelera

Muhammad

Kukakana show kumbali ya ine ndikuona kuti apanga bwino pa chifukwa traole akuzondedwa ndi ma iko ambili nde ngati Burnerboy atapangitsa show kumeneko ndpo ndkukhala ya ulele maiko enawo utha kukhala mwayi wawo olowera kupangaza traole chifukwa chizikireni kuti avomere akuyenera akapezekeko traole ku show imeneyo nde sibwino kutelo manganizo anga

Chrispine nyirongo

Hahaha 🤣

Oliver

Taraore wachita bwino kukana, we are busy building our land, so tizamuitana bwino Boy wanuyo tikakhazikika

Innocent Kalua

A Traore sanalakwitse coz burna boy akanapangitsa show ma haters a traore bwez zawapweteka ndipo akanakulitsa jealous yawo pa traore zomwe zingabweretse nkhondo

Bright

Wachita bwino kukana kumene iyeyo a kuzwa kut nza satanic izi and ma youth ambili amabalalika ndi zinthu ngat izi for example anthu kumwa mowa ku show mwauchidakwa etc koma so munthu akukonza dziko nde Ena abwele azisewelamo zuoneka ngat za nthabwala

Zaiah

There might be high chances kuti ADANI OYELA KHUNGU alowelelepo nkupanga chipongwe TRAORE, wachitabwinokukana

Vincent church hill

Apule sakunama

upload your music with us to get maximum reach out!