Article
Atsikana adandaula kuti ma dating site, mukuchulukila amuna afupi afupi.

Atsikana adandaula kuti ma dating site, mukuchulukila amuna afupi afupi.

Nkhani ya chisoni kwa anyamata omwe Ali ma short, Atsikana adandaula kuti ma dating site, mukuchulukila amuna afupi afupi.

Pamene anthu ambili ali busy kufuna chikondi kudzela ma dating site ngati Tinder, 265 dates ndi ena ambili. Atsikana akhala akudandaula kwambili kuti amuna ambili amene akumapeza pama site wa akumakhala afupi afupi kwambili. Kotelo zikumavuta kuti awakonde.

Mwachidule zikuoneka kuti atsikana ambili amuna afupi samawakonda, ndiye Tinder yaganiza zopanga po kanthu kuti asangalatse ma customer awo. Ndiye kuyambila pano, Tinder yayika filter yomwe izidziwa kufupika kwa mamuna kudzela pa chithunzi kuti atsikana azidziwilatu yemwe ali wa type yawo.

Ndiye kuti Apa anyamata amene ali ma short ali mmadzi, nkhani yomvetsa chisoni kwambili. Tikukhulupilira omenyela ufulu apanga po kanthu, chifukwa amuna afupi nawo ndi anthu.

Kwasala tizangomva amuna afupi aletsedwa pama dating site. Zosayenda

Admin Jeffrey

Comment Below

upload your music with us to get maximum reach out!