Article
Galimoto yomwe iziulukanso yapangidwa, mtengo ndi tsiku lomwe ituluke ili munsimu.

Galimoto yomwe iziulukanso yapangidwa, mtengo ndi tsiku lomwe ituluke ili munsimu.

Galimoto yomwe iziulukanso (flying car) yapangidwa, mtengo ndi tsiku lomwe ituluke ili munsimu.

Pamene nkhani yi yakhala ikukambidwa ngati nkhamba kamwa chabe, company ya Klein Vision yalengedza kuti yapanga galimoto imene iziyenda pansi komanso kukwanitsa kuwuluka bwinobwino (flying car), tikukamba pano zithunzi za galimoto yi zatuluka kale ndipo ena akuti ayiwonadi ikuwuluka.

Ndiye kuti ku tsogolo ku, munthu oyendesa galimoto ayamba so kukhala pilot wa ndege yekha. Nkhani yaikulu imene anthu akhala akufuna kudziwa ndi mtengo wa galimoto yowulukilayi komanso ambili adabwa kuti koma izi zingakhale zotetezeka?

Galimoto yi akuti ipedzeka pa msika kumayambiliro kwa chaka cha 2026, ndipo mtengo wake uziyambila $800,00 to $1 million (yomwe ili kudusa 1 Billion Malawi kwacha)

Komano pachi Malawi nthambo za magetsi ziilikuno komanso ndege za makolo za usiku, zilola technology imeneyi iwadyele shine?

Admin Jeffrey

Comment Below

38 Comments

2026

2026

2025

2026

2026

2026

2025

2025

2025

2025

2025

2025

2026

2025

2026

2025

2026

2026

Blackson

Simmene kulili

Fikhy

Technologia

Clinton Batani

😂️ 😂️ tekinoloje

Plug smoke

😂😂😂

Mathews brown

Ndipo zodyerana shine sitikulola. Tikumana mmalere momo 😂😂😂😂

Rigoodreo

Anthu ambir amwalira nazo izi 😔

Noic

Idzauluka bola ifike🤣🤣🤣

upload your music with us to get maximum reach out!