Uwu ndiye u friend weniweni osaona nyengo
Ma picture atsikana ali pa Wheelchair uyu akupanga circulate kwambiri pa social media pano ndipo titapanga research tapeza izi
Atsikana awiri awa ndi ma friends kuchokera kale kale ndipo school anaphunzilira limodzi mokuti ali pa Wheel Chair yo dzina lake ndi Zama Nxumalo anabadwa wabwinobwino Koma anachita ngozi
Ngakhale pano samakwanitsa kuyenda Koma nzakeyo sanasiyebe kucheza naye monga mene amachitira kale ndipo pakakhala chisangalalo amayesesa kuti apite akasangalare naye mutha kuona picture inayo ali limodzi pa Christmas onse atavala zofanana
So chimene chasangalasa anthu ambiri ngakhaleso mwiniwake wakhala pa wheel chair yo ndichoti nzakeyo anamuuza kuti akupangitsa ukwati ndipo akufunitsisa kuti iyeyo azakhale wapambali pake Ndipo iye atamva amaona ngati ndi ma jokes kenako anadabwa akumamufunsafunsa kuti Koma ukukonzekera za pa ukwati wanga pajatu uzakhala wapambali panga then iyeyo anazayankha kuti ndizakhala bwanji wapambali pako Ndili pa Wheel Chair? Koma nzakeyo ananena kuti sikuti mene ndimakuuza kuti uzakhala wapambali panga sindimadziwa kuti unalumala Ndipo ukumayendera wheel chair I know all those and I repeat you will be my bridesmaid in that Wheel Chair
Fast forward below are the pictures of her as bridesmaids to her long time friend while on a wheelchair, Chikondi chosaona nyengo chija ndi ichichi
Nzako azikupats mtendere
Who is cutting onions here😭😭😭
Zosililisa zanko azitero ndithu ,bwez lisamawone nyengo yomwe uli
Friends of benefits indeed
Ine i once had a friend who truly loved me Cynthia Mdachi, unfortunately tinasiyana form 3 she went to a boarding school, it was heartbreaking coz she was the one for me 😭
Zosangalatsa ❤️
Zosangalatsa ❤️
Zosangalatsa ❤️
Sungamazifile lonely apaso, ndiochepa angapange izi
Bwenzi losaona ulumali, akamati Umulungu ndiumenewo chikondi cheni cheni .
Okay
Zosangalatsa kwambiri bwenzi lenient lizitero
Ok
Best friend for real
Impressive
Bwenzi losaona nyengo ngat MASM.
Bwenzi losaona nyengo ngat MASM.
Bwenzi losaona nyengo ngat MASM.