Chifukwa chimene President wa ku Burkina Faso wapangira Bun ma video ndi ma website olaula dziko mwake
Tsopano President Ibrahim Traore officially walengeza kuti Wapanga Bun porrrrn videos and websites dziko lawo la Burkina Faso
Izi zikutanthauza kuti ma citizen a ku Burkina Faso sazitha kapena kuti sizimatheka kupanga search ma website kuti aonere ma video akusaweruzika
Malingana ndi Ibrahim Traore akukhulupilira kuti ma website ndi ma videos akusaweruzika aja amasokoneza achinyamata kaganizidwe kazinthu mu zinthu zosiyanasiyana
Ibrahim Traore wati kale kale lija mwinako zinali zabwinobwino chifukwa ma phone kapena amapezeka ndi akuluakulu okha okha koma pano kubwera kwa Technology ndi ana omwe akumakhala ndi phone adakali achichepere kwambiri kotero pena ukangoyasa data pa phone pakopo olo usanapange search koma pamabwera zithunzi zovula zimene amakhala ma advertiser achita kuziikapo mwadala ndipo iye wati zinthu ngati izi sizoona kuti ana aziziona zili ngati kuphwanya ufulu wawo komanso kulowesa pansi culture yathu ya ma africans
Traore anapitilizaso kunena kuti malo moti wachinyamata azikhala busy kuganiza zamoyo wake kuti angatukuleso bwanji dziko lake sizoona kuti azipanga spend more time on internet kuonera ma video akusaweruzika aja kotero tsopano iyeyu wachita bun ma website onse oterowo pofuna kuteteza maufulu a ana omwe akumagwiritsa ntchito internet adakali aong'ono pa zinthu zokhunza school osati zithuzi zovula kumangobwera pa phone pawo olo ngakhale asanapange search ngati mene zikumachitikira masiku ano
Komatu ngakhale izi zili choncho anthu ena mdziko la Burkina Faso sanasangalare ndichiganizo chimenechi pakuti akuti iwowo popanda ma video komanso ma website akusaweruzika sangakhale ndipo moyo wawo uzisowa kenakake
Inu maganizo anu ndi otani pa chiganizo Cha Traore chochotsa komanso kubana ma video ndi ma website akusaweruzika? Chitani comment timve kuti Kodi ku Malawi kuno mungafuneso zitatero?
That's the way to go..
Wachita bwino mavedio oluula siabwino kwa munthu wina aliyetse chifukwa ayabitsa chisebwere
That mn is my favorite
Yes monga ngat one nde ndagwilidzana nae traole ndganidzo lozamali ndi I would like kut ife monga aMalawi tikanakhala nd apule onkhwima maganidzo ngat traole mmmm ine apaaaaaaa!! Dziko lanthu lija bwedz tikulimva kukoma heavy
Zingathe kuthandiza kwa achinyamata kuchepesapo mchitidwe ogwririra
Nchifukwa kuli ma VPN
Ku Malawi ๐ฒ๐ผ kunoso akanabana tikanasangalalaso kwambiri
Zitachitika kumalawi kuno zingakhale bwino kwambir chifukwa ngakhale kuno so Ana Ali ndimaphone ndpo zimenez zikuchitika...
Chifukwa chan anthu oterewa sali akuno kwathu kunali magufuli apa uyoso traore koma kuno maloza okha
Kunonso apange bun
Amakwana koma. Zichitikenso kuno ku Malawi
Amakwana koma. Zichitikenso kuno ku Malawi
Amakwana koma. Zichitikenso kuno ku Malawi
The brotherhood is proud of you Ibrahim ,,,keep it up
Mtsogoleri koma ameneyu
That's a nice move TRA, indeed porrrn videos lead to downfall of African culture.
Ngati kuli president yemwe akufunila zabwino anthu ake ,ndiye ndi Traole,akuona kufunikila kolemekeza ufulu wa ana mdziko mwake.Ndichifukwa chake tikaonetsetsa mdziko la Bukina Fanso zinthu zikuyenda bwino kamba kautsogoleri wamasomphenya.Kwaiwo omwe akuti sangakhale opanda mavideo akusayeluzikawo,akadakonda akadzifufuza kuti kodi kwa iwo vuto ndichani.
I like Traore wise guy and God fearing man. God why not Malawi ๐๐๐ค
True definition of a leader who lead by example
Chiganiza chabwino chimenechi sakunama ayi coz zimachotsaso uzimu
Wachita bwino sanalkwise
Nice decision amuna traore
Traore uja simunthu wamba ndipo that decision akulu ndiyabwino koopsa but us people canโt see that.....
Mashalllah ๐๐๐
Thank you for recognizing for that opportunity to add my comment here in this box , inshort Ibrahim Traore has it good , and if this can proceed here in malawi it can as well help the reduce of bad behavior of indulging on early sexuals and reduce of deaths caused by young โค๏ธ broken of under aged boys and girls ( teens)
Zili
Idea is concrete...I like it ..I wish ku Malawi kunakakhala choncho coz many youths are being taken down mentally coz of pornography and musterbation.
Chiganizo chokoma kwabasi chimene President Yu wapanga m'dziko mwake. Moti ngakhareso kuno ku Malawi kuno ndi zokomaso ndithu, zitakharaso kuti zachitika motero momwemo kupanga burn. Chifukwa zinthu izi zili ndi cholinga chofuna kulimbana ndi moyo wa uzimu kuti usamapite chitsogolo mu miyoyo ya anthu. Ndiyeno chifukwa ca ichi zingakhareso bwino kuletsa ku burner kuno ku Malawi.
ndipo or atachotsa lero miyoyo yathu itha kusitha kwambri. pa phone titha kumakghala busy ndi zithu za phindu monga ma business kupanga ma practice zithu zosiyana siya. pamene ma porn ndi zithu zomwe zikulepheletsa athu kupita patsogolo ndo internet. chitsanzo ineyo almost my life panopa ndimadalira internet kuti didye koma 2 munits ina yake ndimazasiya za business ndikuyamba kupanga zoonera zimenezo chifukwa cha advert yeni yeni.
Ineyo ndikuona kut Traore ndi president ofunila zabwino dziko lake komaso ali ndi chikhumbokhumbo chodzafuna anthu ake komaso iyeyo onse adzalowe kumtendere wamulungu
Yah ndimaganizo anzeru kwambiri Ndipo tili pambuyo pake
Waganiza bwino kwambir ndipo mulungu azimudalitsa
It's a gud development
President wanzeru kwambili
smart decision...
Bun
Ndipo sanalakwise zimenezi zumalimbikisa chiwelewele kwambili Pano kukwelana kunaphweka chifukwa anthu akumayenda Ali ndi zibaba kale Kuzela pakuonera ma video asagaduzowa
Kwathu kuno Bora zikanatero mwna kukharako mw wasogoro labwno
Ndi president oganiza ndie ameneyu,ndi zoona achinyamata akutaya nthawi kuonera zopusa,ifenso zitatelo zingathandize kwambir
Yah zilibwino chifukwa zimatisokonezadi achinyamata mix panopa or ma ads akabwera amakhala atsikana ovula zimene munthu zimakupatsa attractive kuwonera porn ndikumabunyura zimene zili tchimo pamaso pa Mulungu ndiye kunoso ku Malawi atapanga block zikhoza kukhala bhow pat
Maganizo abwino kwambiri ndipo maiko akwathu kuno Ku Africa akanachita ngati mene wachitira Ibrahim bwenzi zili bwino koopsa
President traore waganiza bwino kwambiri
Wachita bwino sanalakwise
Kunena fact zinthu zija olo kunoso atachotsa palibe vuto coz zimapanga drain mindset ya achinyamata timakanika kuganiza zolongosoka
Ndipo kwambili kunoso zchtike
Kupanga bun ma websites ama porn, ndi chinthu chabwino chifukwa ana ambiri masiku ano akumayamba zogonana akadali achichepere kwambiri nkumatenga mimba zomwe zikupangisaso kuti azisiyira school panjira nkukalowa ku mabanja ali ang'ono kwambiri. Wachinyamata ameneyu sangatukule dziko lake ayi. Nzofunika ndipo nzabwino ngati Malawi itatsatila chiganizo chimenechi. Zikomo
Izi zilibwino Kwambili end ndi chiganizo chabwino
traore tsadalakwitse fkwa akufna kukonza zne otsat kuwononga zn2 ngat m'mene zkuchtkir nziko la2 lino
Great idea Mr President mkanakonda kunoso akanachita zomwezi๐๐๐๐๐ ndili paselipa
Uyuyu ndi msilamu weni weni And We need this kind of leadership in our country
It It seems that Traore is a very good president, especially when it comes to making decisions. This decision is good and will help reduce prostitution in the country.
Maganizo abwino kwambir
It's a good decision and I proud of him, technology must have some measurements like this so that our youth can concentrate other good things not just wasting time for stupid things
That's gud I dear brw
Wichita boh
Yeah โบ๏ธ I do agree with him
Izi ndiziona ndipo ine ndikugwilisana nazo cz kt muon pano ana ambili analowelera cz anayamba kuziona ali achichepele izi zikufunikaso kumalawi kuno pano Mwana wazaka 15 akumakhala ndi Mwana mzake chifukwa chazimenezi chiganizoo chabwino kwambili
Eya wachita bwino...
Ndipo kwambili that's why dziko lathu likupita patsi chifukwa chakuganiza popelewela komwe azisogoleli anthu Ali Nako thawi yayitali ikumathela pa ma porn chomcho angaganize zithu zotukula Malawi??
He is a wise b4 becames presidential state , i support the genius idea he rare things abroad indeed that kind of behave he does is very scarcity in africa , may humble God continues bless his ideas ๐ค๐ฅ๐
Traore is a hero end he know how to hand the world ,coz this website is disturbing more children and more youths ,for example the increasing of rape one of the cause it's porn
this is the example of a living president am supporting it โ โ ๐ฅ
๐๐sangakhare nd mogo?
It is a good decision and ndukusapota mfundo imeneo
Eya wakhoza I wish tikadapangaso tero
Adha aja ndi genius idont bฤบame him for every decision he makes
Apanga bwino kwambilitu achinyamata akubunyura kwambiri
Yes that is good desertion to the country Ndipo ku Malawi kunonso zikanatelo zikanakhala bwino kwambili
Ayi samalakwitsa wapanga bwino kwambil zimaonengaso Ka ganizidwe kwa ana zimenezo coz amat tikaesele uona zot mpaka atenga nazo mimba
This is great movement, God is with him Traole๐
Yap. Maganizo abwino kwambir. Ndngakondwenso zitatero kathy kuno
Ndi dolo kangapo ameneyo kunonso I wish atapangaso burn ndthu
Kod ma president athu kuno Ku Malawi sangayesele kukopela izi??? This guy is a genius ๐
Ineyo to say the fact; mfundo iyiyi 106% ndugwirizana nayo kwabasi ndithu, coz iyayi anthuwa akumaonjeza kwabasi sizoonayi izi
The decision is as massive as Gold. We don't need porn in Africa. Young men spend much of their time watching nonsense on internent and getting no penny in return. The one who posted it gets a lot of coins but the one watching it gets nothing, what's that game?! We need young people who can think of how to have their social lives developed, not being addicted to foolish things like ponos, big up Traore, one day the whole Africa will bun intetnent and be like the 1800s, just to redeem the young generation. I believe that will happen one day.
Uyu nde president oganizila komaso odziwa ubwino ndi kuipa kwa zinthu zina pa ma citizens ake...
He is a leader, leading a better future for the kids who will be the future leaders
Well done Mr president, ndipo ndi zinthu zonyasa kumene kumaona zinthu zolaula congratulations Mr president
Apapa ngati zingapitilire,dziko la burkina faso likhalanso la anthu okhulupilira Mulungu kwambiri,long live Ibrahim, Kumalawi mwina titapereka mwai kwa bwana TULI atha kuchitako pang'ono
Apap nxen waith aaa zimatisokonez kwambir aaa
Chilungamo ukupweteka akhalitse ameneyu
President uyu ndi oganiza kwambiri komanso zikuonetseratu kuti akudziwa mavuto amoyo wa munthu mma levels onse, NDI pemphero langa kuti Ambuye atichotsere chitsiru tili nacho ifechi ndikutipatsa munthu oganiza mwakuya ngati president Traore
izizi ndzimene zkufunikaso ku mkalawi kuno kodi tkukanikiranji kudzuka ngati traore?
Zinthu zabwino kwambiri
President of the world, he deserve the chair ๐ซก
Nanga zabwino zipose apaaaa waitha Traore
Ukuku nde kuganiza bho coz azungu aja aapanga ma video akusaweluzika ndicholinga chofuna kutichedwesa, kma apapa mayuthi ambiri ku Burkina Faso ๐ง๐ซ akhala busy nd zinthu ziti ziziwapindulira...i wish Traole akanakhala wathuwathu ku Malawi ๐ฒ๐ผ kuno
Aaaaaa anthu amene akutsutsana ndi zimenezo akulamulidwa ndi ziwanda kumalawi kuno adakatero zinakatichitila ubwino ๐
Ndi nzeru komamaso umunthu
Waitha koma kaya Malawi ikukhalira pati kaya
Apa tipanga ndalama. Tiziwagulisa ma citizens aku Burkina Faso wo through WhatsApp or Email. Tipha makwacha
Walakwisa ibrahim coz ma porn ndi feel komaso njira imoz yopewer sex ngt sukufuna kumana ndi nkaz umango streamer ma porn nkuzthandza wekha
That's good idea
Wise decision๐ฏ
Akhalise Ibrahim traore ife ma African timaziwika bwino ndi chikhalodwe ndye nzofunika kusunga chikhalidwecho God bless Ibrahim traore forever and ever
Perfect
asadandaule tiziwatumizila pa wap
fixing the country in good way.. mindset change first
Traole has done a very remarkable job to his citizens. Pornographic clips destroy minds. If I had time to speak to him I would also advise him to ban gambling, both physical and online gambling ( aviator) eeshi mchipembedzoso icho
Zofunika kom izi
Traore to the world smart guy all over world
This president is genius. I wish nkanakhala Burkinabe
๐ฌ๏ธKUNOooo!!!๐จ Tasangalala namuza ndinetu
Kopangira ban kuno kulibe????
Kunonso apange bun ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ
Ichichi!!! Chipweteka ma presedent azake chikuganiza mwa nyo!!!!!!
Tipange WhatsApp group ndiziwagulisa anao
Ndipo Traore akhalitse ๐ฅ๐ฅ๐ฅ
I think this guy he's more careful on his kind cause being a reader you have to take risks and don't expect all the pple to love you but it takes an ignorant person so see this as a burden but truth to be told shout out to Ibrahim
Uyu nd dolo uyu
Uyuyu akanakhala kuti Sali pa banja kanapasa sister wanga Bwezi inu mukunditcha mulamu wake wa Traore
I think this president indeed wants good things for his people, especially youths coz exposing pornographies to youth affects them both mentally and physically. I wish if our president here in Malawi copy that style
Ichichi ndi chiganizo chabwino, chifukwa sikwabwino kumaonera zinthu zomwe zitha kukusokomeza ubongo, kuno kwathu zitatero zingakhale bwino kwambiri, komamso ana ambiri amakhala osalemekeza makolo chifukwa CHOTI amakhala akuwadziwa mmene alili
Wachita bwino.chifukwa izi zithandiza kuti, achinyamata akhale ndi nthawi yotukula dziko lawo. komanso kuphunzira zinthu zomwe zingawanthandize pa moyo wawo, pamene akugwilitsa makina a Internet.
Apa ndpomwe ndaona kt traore yu ndi dolo kangapo
Wachitabwino kwambiri chison ndichakut kwathu kuno sanapange olo mpang'ono pomwe
Maganizo abwino kwambiri
Wachita bwino
Amen
Achita bwino, Zidzenso kuno zimenezo
Sanayiphonye wachita bho kwambili kunoso achose
Koma uyuyu Nd shasha
Chiganizo chabwino kwambiri
Eya achita bwino kutero
Wachita bwino
Achita bwino cos achinyamata ambilife imatipweteka ndi peer pressure kuno kumalawi zitatero zitha kuchita bwinoso
Achita bwino kwambiri
Dziko lose lapas titakhala ndi anthu ngt awawa zinthu zintha kumayenda bwino kwambiri zed wachita bwino kwambiri
Just good and perfect idea though some will fund alternative to find them despite being bun on the internet for them. This will just reduce availability of the videos which will reduce exposure to many individuals. Watching while young just induces youths to think that sex is the best thing ever they can plan of hence in their development plan they mix with sexual plans which leads to reduction in the performance of development plans for them. Mapanga awiri avumbwisa
Good ideas ๐ฅ๐ฅ๐ฅ
Izizi zokomera tili ndakazi ambilife koma zitabwera kuno ndili gulu lozikana sure ๐คง๐ฃ
I think wachita bho kwambiri,,staff ija ngakhale Kwa munthu wankulu imasokoneza kaganizidwe,, alesenso online gambling.
Dolo
Gud decision ๐ MashAllah traore
Uyu ndi shasha wenwen