UTHENGA WABWINO KWA MA FANS A MAN U, PA FINALS IMENE AKUMENYA NDI SPURS RELO
Pamene madzulo ano kuli finals pakati pa Manchester United vs Tottenham Hotspurs. Anthu mma group a Man U ayamba kulimbisana mtima kuti asadandaule game yi awina kale akatengela mbili.
Iwowa akuti mu chaka cha 2016 tsiku ngati lomweli Man U inatenga FA Cup ndiye 21 May ndi tsiku lawo la mwayi. Komanso ena anabwela ndikuonjezelapo kuti player Casemiro sanaluzepo finals ya UEFA Europa chiyambileni, kuteleko akuti squad yonse ikudalira Casemiro kuti awanyamule pakuti finals ili relo ndi ya Europa yomwe kuli kudya kwake.
Koma chikuwakaikisa a ganyu akuti Manchester United ma game ake onse amene yakumana ndi Spurs inaluza. Ndiye aganyu akuti ngati Man United yaluza ma game okwana atatu ku Spurs chawo palibe, ndipo aganyuwa achenjeza anthu kuti ngati ndalama zawo sakuzifuna ndiye ayesele ku betela Man U.
Tikunena pano debate yavuta mma group a betting, pakuti n'zathu wina anati "history is the best teacher" ndiye apa history yakolana.
Inu Mukuona kuti ataduse ndi ndani kuwina finals imeneyi? Ndipo mwakwela iti?
Manchester united ikuwina game imeney...it's not about kudzilimbsa mtima kom direct prediction..
Manchester united will win Europa league final spurs lose
Tottenham Hotspur win and over 2
Manchester united will win tonight 🙏
My best team Man united wooooyeee🔥🔥🔥🔥moto kuti buuuu
Manchester iwina