President Trump wayambisa beef ndi oimba Taylor Swift.
President Trump zikuonetsa kuti zosungila mangawa samapanga nawo, ndipo anthu sanayembekedzele iwowa okhala president kumalimbana ndi anthu pa social media. Iwowa analemba post yonena kuti kuchokera tsiku lomwe iwowa analengeza kuti Taylor Swift amawanyasa, oimba yu anasiya kubhebha.
Nkhani yonse yi inayamba chaka chatha pamene oimba Taylor Swift anali mmodzi othandizila campaign Kamara Harris yemwe ankapikisana ndi a Trump pa zisankho zawu president chaka chatha cho. Ndiye izi a Trump sizinawa sangalase pakuti ankamukonda kwambili oimba yu. Ndiye ku muona akuthandizila m'dani wawo pa campaign anakwiya ndi kulemba post yokuti "I HATE TAYLOR SWIFT" pa 15 September, 2024.
Ndiye dzana pamene anali kuchokera ku trip yawo yaku aluya, anangoti akumbusile ndi kulemba uthenga pa page yawo ya Trump imene inali mu chizungu chokuti "Has anyone noticed that, since i said " I HATE TAYLOR SWIFT", she is no longer "HOT"?
Mokuti ambili aweluza president pa khalidwe lawo li, akuti amakonda kunyoza azimayi ndipo uyu si mzimayi oyamba kumunyoza. Ndipo owayankhulira a Trump ku white house anayankhapo kuti a president wa sikuti amanyoza koma amatanthauza kuti sakubhebha ku nkhani za ndale osati maonekedwe ake kapena nyimbo.
Pamene oimba yu zikuoneka naye so anawayankha a Trump wa mu nyimbo yake yotchedwa "You Need to Calm Down"
Pamene anafotokoza kuti "You are somebody that I don't know
But you're taking shots at me like it's Patrón
And I'm just like, "Damn! It's 7 AM"
Say it in the street, that's a knock-out
But you say it in a tweet, that's a cop-out
And I'm just like, "Hey!
Are you OK?"
Beef yavutaso, mpaka ma president ndi oimba, Inu muli mbali ya ndani?
Trump penapake mutu wake sumagwira
Trump
Koma yaaa trump mutu sugwilad😂