Article
Chifukwa chomwe Burna Boy akufuna ampatsire ndalama Ibrahim Traore

Chifukwa chomwe Burna Boy akufuna ampatsire ndalama Ibrahim Traore

Oimba wa ku Nigeria Burna Boy walonjeza kuti amupatsa ndalama President wa ku Burkina Faso

Tisanaifotokoze nkhani yonse Funso mkumati Koma izizi ndizoonadi oimba mpaka angafike size yopanga challenge kuti apereka ndalama kwa President wa dziko? Kodi kapena yawo ija ma artist ma stunt?

Tiyambe ndi mtengo omwe Burna Boy ama charger per show, Malingana ndi kafukufuku emwe ali pa internet ndiwoti Oimba wa ku Nigeria yu kuti akaimbe ku show yako amalipilisa ndalama zokwana 1 Million US Dollars komanso kupatula pamenepo umayenera kuti umulipilire private Jet yochoka kwao kukafika komwe kuli show zimene ndalama zonse ukaziphatikiza zimakhala zambiri

So now let’s get to the bottom of the story, Pamene Maiko ambiri muno mu Africa akuyamikira ulamuliro wa President wa ku Burkina Faso Ibrahim Traore indedi ndizoona naye Burna Boy walilonjeza dzikolo kuti alipangira zinthu izi posafuna anything in return

Burna Boy walonjeza dziko la Burkina Faso kuti apitako kukapangitsa Concert kapena kuti Show yoti samulipira chilichonse ndipo ndalama yonse yomwe itakapangidwe ku Show imeneyi yonseyo azaipereka kwa President Ibrahim Traole kuti ithandizire kugwira ntchito za Chitukuko zomwe President yu akupanga kale Mdzikomo

Padakali pano Ibrahim Traore sanayankhurepo chilichonse pa nkhaniyi Koma Burna Boy ali ready Ndipo akuthokoza pa ulamuliro wa President Traore posintha kaganizidwe ka ma president ena ambiri muno mu Africa

Admin Jeffrey

Comment Below

58 Comments

2025

2026

2025

2026

2026

2025

2025

2025

2026

2026

2026

Sydney Maiden

Great

Hope Kaliwo

Mumatha

Marco mgemezulu

Thus great idea

Morgan

Izo ndizofunikira potengera umunthu womwe burn boy alinawo 🙏🙏🙏🙏🙏

NANDOLO

Apo ndiye titha kunena kuti Africa yabwela sopan

Falook cassim

Eee kungot Ibrahim traore ndi president wodabwisa zochitika zake km khani iyi traore alola kt athandize potengera naye burna boy ndi waku africa 🌍 nde achita bwino akatelo

Precious Matako

Nthawi yoti MA afilikazi agwirane manja ndiyiyi

Justin Makhela

Zosangalasa kumalimbikisana

Hackson

It's okay, because the money he gonna gain in his show will benefit the country of Burkina Faso.thats great 👍

Ibrahim Traole

Burna Boy ndiDolo

Blessings

Zlibwino heavy

Alli Omer

Amakwana Burna

Harold

Burna boy cover🙏

Harold

Burna boy cover🙏

Jhanga Bosco

Akachoka kumeneko azakomaneso nd chakwera ku malawi kwanuko

Jhanga Bosco

Akachoka kumeneko azakomaneso nd chakwera ku malawi kwanuko

Jhanga Bosco

Akachoka kumeneko azakomaneso nd chakwera ku malawi kwanuko

Jhanga Bosco

Akachoka kumeneko azakomaneso nd chakwera ku malawi kwanuko

Jhanga Bosco

Akachoka kumeneko azakomaneso nd chakwera ku malawi kwanuko

Jhanga Bosco

Akachoka kumeneko azakomaneso nd chakwera ku malawi kwanuko

Vyete

Bola asakhala kuti watumidwatu uyu

Donald Trump

This president akufuna ndimuphe

SKENZQ-K

Ok

Kondwani kachikuwa

So nice

Raphael Limau

Koma nde manthanyura akuyenda malondatu🤣🤣🤣

Esthernkunga

That's powerful

Sam Nderema

Let's appreciate what our fellow Africans are doing osamangosapota azunguyi

Davie chikaonda

That's powerful every one needs gift

Jimmy Bonongwe

That's great everyone needs gift

Vincent Zaliwa

I like this forum

Rawlings web ghandi

Yàaah it's good, don't mind far

Gee higa

Burna ndi African gient

Victor Chidothi

Amutuma akatero

Frezzeir the huntre

Watumidwa

Nyambi

Watumidwa ndi trump uyu sure

Samuel khembo

Uyu nd dola athad kupeleka

Crystal diver

Ibrahim traore he is a good leader

Chakwera

Nane Niluyenera Nipiteko Uku

Harold mailos

Thank you for the support and help with your gift

Enerst R chiphwafu

Zilibhoo km asamutengele ku mtoso paja mati mkazi amadya Ibrahim trore nayeso burna boy amalowama

Astro k mw

Nzeru

MISHECK

GREAT THINKING

Peace maker

Zili bho

upload your music with us to get maximum reach out!