Zinsisi Zodabwisa zimene Eli Njuchi waulura mu album yake ya CIFU
Eli Njuchi ndi modzi mwa ma artist okhawo amene ma project awo ngati ma album kapena EP amakhala ochitisa chidwi, kotelo watulusa ma album okwana 4, pamene ya chi number 5 ndiyomwe watulusa lero ya 'CIFU'
Pali zinthu zingapo zomwe zachititsa anthu chidwi komanso zina zomwe munuwake waulula mu album imeneyi.
Ndi chifukwa chani pa album cover ya CIFU wagwilitsa ntchito chithunzi chimenechi komanso cha makhalidwe otelo?
Yankho mkumati, kwa onse amene akudziwa bwino album cover ya Eli Njuchi ikufanana ndi album cover ya Michael Jackson thriller (yomwe inatuluka 1982). Sono tanthauzo lomwe amafuna kupeleka pa chithunzi chi ndi chakuti tsopano Eli Njuchi akukhulupilira kuti wafikano podziwika bwino ndipo akuthokoza pa support imene anthu akhala akumupasa (pakuti album ya Michael Jackson inaliso ndi tanthauzo ngati lomwelo atatchuka kwambiri
Gawo lachiwiri tiloweno mu nyimbo zomwe zili mu album yi, komanso chinthu chachikulu chimene Eli Njuchi waulura ndipo anthu akhala akudikila kumva mbali ya moyo wake
Zikuoneka kuti Eli Njuchi wapeza nkazi ndipo wamufotokoza kangapo nkaziyo mu nyimbozi ngakhale kuti sanamutchule dzina chifukwa wazifotokoza mozembayisa, koma ife tadziwabe funso mkumati inuyo makosana zimenezi mwadziwa bwanji? Dikirani tikufotokozereni motere
Nkhani zonse zinayamba ndi nyimbo yoyambilira mu album yi, yomwe waimba ndi Malinga Mafia pamene anafotokoza kuti ex wake panopa akumulira njuchi, ndipo nyimbo yotsatila ndi imene inafotokoza kuti akumulira iyeyu chifukwa chani?
Nkhani yeniyeni yomwe yapangitsa kuti ziululike zonsezi ili mu nyimbo number 3 yotchedwa TRUE LOVE yomwe Njuchi wabwela poyela kuzanena kuti pali mtsikana amene wamupengesa ndipo iyeyu ali mu chikondi ndithu, Eli anaonjedzela kunena kuti mu galimoto yake ija chimene amanyamuliramo ndi chikondi basi osati katundu aliyense kapena anthu achisawawa.
Mu nyimbo yomweyi wanenanso kuti iyeyu samamwa mowa, ndipo tsiku lina a police a (breathalyzer) oyeza anthu oyendesa galimoto atamwa mowa atamugwila, atamugwila ndipo atamuyeza ndi chikondi chokha anachipeza nthupi mwake.
Zachikondizi mu album yi zapitiliraso kukambidwa mu nyimbo ngati MASIKONO komanso COMPOSURE Komatu iyeyu anafotokozanso mbali ina kuti chikondi chi pena chikumasokonekela ndikukanganampaka Njuchi kumaopa kupita kwao Komwe, ndipo mpaka nyimbo yomwe waimba ndi Lulu inali yofotokoza kuti iyeyu ali DISAPPOINTED pakuti chikondi ndi chovuta koma chomwe cha tsangalasa anthu chakuti tsopano zaziwika kuti mkulu yu wayamba kupanga Zachikondi atakula paja chaka chatha wakwanitsa zaka 23, wakula ndithu.
Koposaposa album yi, ili ndi nyimbo zina zomveka mwa Gospel ngati WEKHA, koma monga mwachidzolowezi waimbamoso ina yolilitsa komanso yokhuza yomwe ikukamba za mayi wina yemwe ntchito yomwe amagwila simadziwika.
CIFU Ndi album yosafuna kumvela uli ndi phuma, yapangidwa mwa luso komanso muli zinthu zambili zokuti utha kupanga relate. Ndipo masiku akubwela wa ijayo ikukamba zokuti osamabisana ngati thumba la chamba, tiyamba kuiona muma TikTok mu.
Osaiwala mutha kukaipanga download kuti mumvere nokha podzela mu link ili munsiyi, mukamveka tiuzeni kuti inu mwaimva bwanji?
DOWNLOAD ELI NJUCHI NEW ALBUM "CIFU" π
https://makosana.com/pack.php?album=Cifu
Eli njuchi palibesoπβ€
He is tale3
My favorite artist Eli njuchi on fire π₯π₯π₯π₯7οΈβ£
Eli njuchi ndi favorite artist wanga mpaka kale amatha komaso amandiwaza π₯π₯π₯
Koma nde kufotokoza momvekatuπ₯
Song ya Ntchito ija ndayamba kupanga relate apapa. Zotheka bwanj akuntchito osabwera pa Maliro. Mayi ameneyu amagwira ntchito yanji?
Uyu atikomola ndithu
Dolooo ka4
Dolooo ka4
Eli Njuchi matha, ndidolo kwambiri.
I love this guy's music alot
True love pa repeat
Eli ND katakwe kangapoπ my favorite artist π₯π₯π₯π₯π₯π₯
Thanks Eli iweyo ndi Dolo katatu
Amatha adha awa
album ili mwala iyi
chikazati Njuchiiiπ¦
Ndi super star adawa
OK tadziwa nawo koma ndi solo heavy
OK tadziwa nawo koma ndi solo heavy
Apa ndiye yapeza duwa ndadziwa nao
Nice album
#role_moDel
Giya 4 bas amakwana
Ndipo mwapangisa kt ndiimvesese bwinobwino makosana Ulemu wanu
This is very nice... Tamvamo zambr
Zaphamvu
Mwanayu ni dolo
Zili ngati kale
Massive album timvele mofasa bwino ndinthu
Akuluwa anabwela koma kunena chilungamo komaso osaiwala chizmo uja ndi veda njuchi in one song tinaiva kale
Congratulations Eli Njuchi it begins by a little to make a bunch
π₯π₯π₯π₯
Mfana wa luk shap2 ameneyu maguy kmaso music apa amiyada bhobho nd2 kma πππππ
Eli njuchi is another level of music this guy is awesome ndisaname I'm listening to the album kachikena I'm not done yet
Uyuyu ndi dolo πππππ
Nyimbo ilibho
This is a great album en Eli Njuchi amandipatsa chidwi kwabas, mfana wa look sharp en odziwa life, Respect
The album feels romantic an I really like it
The album feels romantic an I really like it
ELI NJUCHI Is great thinkerπ₯β
Makosana Munthuyu ndi Hero basi π₯π₯π₯β€οΈ
Mwanai ndi dolo
Elli will always be the best
Album ili fire moti tivera Chaka chose π₯π―βοΈ
Album ili fire moti tivera Chaka chose π₯π―βοΈ
Mfana wa luntha kwambiri
Amene tangowerengako First and last paragraph here is a place to gatherππ€£π€£
Nice
Mumuuze adzaniyimbireko mingoliyi ku state house, nyimbo zaluso kwabasi
Amene mwamaliza kuwerenga tapangani summary ππ
Speaking of honest, Eli Njuchi is such a young talented man who every young guy can never run away to be like. At first, I listened to all songs and I was like,... ah! As usual it's just songs. But then when I was listening to it one by one at my leisure time, that's when I related all songs respectively to the current life we are in. I just wish to make amazing music like you broh Eli, such a good work ever....in love with all your music Fadah.
Aaa pa nyimbo yake ya composure komanso kanthumba nyimbo zimenezi zandithuzitsako something π€π€π€π€π
Album ili sharp π₯π₯
Mwanayu nd Dolo kwambri
Ndidolo kwambili
Album nde yaphedwa amakwana njuchi
Γ aaa makosa
Mwanzukutuladi inenso ndimvera album iyi .poyamba sindimanvesesa mwa nyimbo zina coz ine ndikamanvera nyimbo ndimasata chiyambi thutu ndi mathero ake.even inenso nyimbo zanga popeka ndimagwilitsa nchito njira zitatuzi.Elli njuchi ndimamopasa ulemu muzambiri khalidwe komanso kuganiza mwanzeru ndi mozama ulemu wake ulendo wabwino mmayimbidwe ake
Ine akaka kacha 5 ndikuyivelabe modekha km ikukoma ndimodzi komaso pamodzi pen peni kd kwen kwen inuo ikuwazani pat aah ngat ndukuvesan ine πππ
Mwanzukutuladi inenso ndimvera album iyi .poyamba sindimanvesesa mwa nyimbo zina coz ine ndikamanvera nyimbo ndimasata chiyambi thutu ndi mathero ake.even inenso nyimbo zanga popeka ndimagwilitsa nchito njira zitatuzi.Elli njuchi ndimamopasa ulemu muzambiri khalidwe komanso kuganiza mwanzeru ndi mozama ulemu wake ulendo wabwino mmayimbidwe ake
Nosenseπππ
Mbambande