Inde! inu ndi wa ku malawi komkuno uyu kwao Kwenikweni ndi ku Karonga zamuvuta basi
Court lina ku Manchester dziko la UK, lalamula kuti Mβmayi wina wa ku Malawi amene amakhala ku Manchester akakhale kundende kwa dzaka ziwili ndi theka, 2 years 6 months.
Malingana ndi bwaloli Sandra Ntonya amene amadziwika bwino pa facebook ndi dzina loti Andu ndipo amagwira ntchito yosangalatsa amuna othodwa kapena kuti uhule anamunamizira nkhani zokhudza chisembwele bambo wina otchuka amene amasewera masewero a Mpira wa rugby kuti anagona naye komanso kumuyika pa page lake la mchezo la facebook opanda chilolezo.
Bwaloli litamva nkhaniyi koyamba linagamula kuti aunt Andu amene kwawo ndi ku Karonga, asapalamulenso kwa dzaka ziwiri Ndipo asazayankhulenso zokhuza nkuluyo komanso kuti apite ku chipatala akalandile mankhwara chifukwa mutu wake ukuoneka kuti sumagwira bwinobwino koma andu pamenepo anakhala ngati antokosola pabala Ndipo anapitiluza kumunyozabe nkuluyo pa facebook ndi TikTok komanso anati judge wa bwaloli ndi wa katangale kotero wagamula mulandu mokondera
Zaka zina zambuyomu Andu Sandra Ntonya anapalamulanso atamunamizira Prophet Bushiri nkhani ngati zomwezi Ndipo wakhala akukangana ndi anthu odziwika bwino ambiri kuno kumudzi komanso international
Amuchita bwino amuchepeselaso zakazo
Ndie ndiovayatu,kumangokhala kunamizira anthu andalama zawo okhaokha,kutheka ndizoona but alibe enough money kupeza lawyers wabwino
Bola khani iyi ikumveka ngati si stunt
Mmmm anyanya naye aka save aphudzile mwambo no problem ππ²πΌ
Km ndie eeeh
Koma watiyimilila a Malawi fe
Akapume uyu aaaaa
Ookay ookay
Ndezinamuthera bwanji kachikena?
Uhule azimayi enawa eshhh
Azatipeza akatuluka kumeneko tikumudikira kuno
Kuchoka nayo patali mbiri yachabe my gender
Kod tikomentere pati
It's hard though
Different dicks can make someone go crazy π€£π€£
akagobole basi anakondwetsa amwaliwa
Aah andu
Chakwela Aluzaππ
Umhu
Zaka zachuluka
Timuthokoze ameneyo akutiika pa map kkk
Uyu nd team Balabha π
Musamatitukwanitse chonde..... Apa mufuna sympathy from us, Malawians.... Phunzirani kukhala bwino ndi anthu!!!
Zakazo nduona ngat zachepa iyaaa
Ntchto zamanja ake zatchira umbon
yusuflackson1@gmail.com
Yu
Child
Koma ndi dzaka zochepa
Zake zimenezo ππ
Aziona π€£π€£π€£π€£
Nyemba zake ziti zopalamulitsanazo akaziwa akufunisitsa kumwamba kutilake basi
Zauhule basi agwile ndende Ameneyo basi ndiposo galu ameneyu siwakumalawi asatiipisile mbili Ife mudziko Muno Ameneyo akhale wakuzimbabwe basi mbuzi yamuthu
Mbola
Iyaiii ndimisala yomweyo yomwe imamupangisaπππ
It was misunderstanding she tried to make customer care not what people sayingπ€£πππ
It was misunderstanding she tried to make customer care not what people sayingπ€£πππ
Kod akuona ngat kunamizla munthu otchuka mlandu mkuwina ndmasewela et?....π€£ Sungaiphule mophweka ase sewezan ndende chabe kumeneko π€π€£
ππππ kumatiwalira pa Media chosecho ndi hule lacgabechabe πππ what a life
Abroad life be like
Eeeee upakuri wavuta dziko lose adonaπππ
Eeeee upakuri wavuta dziko lose adonaπππ
Zathera ku wire
Andy anapenga
Mwana wa mbumbutera uyu
akutichitisa manyazi ku dziko laeni amafunisisa ndalama zachidule kwambiri
Tengereni ku Zomba uyu π mudikira chan kmnko ma umbom osewa
Tengereni ku Zomba uyu π mudikira chan kmnko ma umbom osewa
Munthu siungazuke ma mawa kumati wandipakula chilipo chilipo aaaaaa maka maka Pa wathuyi ππππ
π€£Oho
Simene kulili
πππkoma aunt andu eeeeh dolo kwambiri π€£π€£
koma zinazi
Zamanyazi
Ndilibe comments
Uyuyu mutu sugwira cox akati atukwane eishπππ