Oimba Tory Lanez athamangira naye kuchipatala ma prisoner anzake atamubayabaya thupi lonse ka 14
Tory Lanez emwe kwao Kwenikweni kuli ku Canada akhala akusungidwa kundende ya Califonia kwa zaka zokwana 10 pachifukwa choombera oimba nzake Megan Thee Stallion ku party mu 2020 ndipo ma ola atatu apitawo athamangira naye kuchipatala atataya magazi ochuluka
Malingana ndi BBC akuti Tory Lanez emwe zaka zake Zili 32 padakali pano chifukwa chakubayidwako akumva ululu ochuluka mβmapapo ndipo amalephera kupuma payekha kotero anamuikira machine othandizira
Tory Lanez ali othokoza a prison staff omwe anamuyamba ndi first aid ku prison komko before taking him to the hospital ndipo malingana ndi oyangβanila ndende ya California akuti ayambapo kupanga investigate guru la ma prisoner anzake omwe anamuchita izi
Kupatula kuombera oimba nzake Megan Thee Stallion Tory Lanez anapezekaso ndi milandu ina yomwe anaikidwa nayo mu ndende mu 2023 ndipo milanduyi ndi monga
(Three felony gun related charges including assault with a semi automatic firearm)
Tory Lanez ndi Megan Thee Stallion anali paubwenzi ogonana ndithu ndiposo kumbali ya nyimbo pena amagwilira ntchito limodzi moti kuomberanaku kunachitika pamene anasemphana chichewa pa ubwenzi wawo wakale ku party pamene Megan Thee Stallion ankayamba ulendo ochoka ku party ko izi ndizimene anafotokoza Megan mu court atafunsidwa mene zinakhalira
Azungu mpaka kusemphana chichewa
ZOSAENDA
Dzovuta kwambiri
Zovuta
Very sad
Musician bad
Koma ndye zovutatu zinthu zakeziiiπ€₯
Zosayenda Kodi timagowona ngt anasiya kuyimbatu ali Ku prison zosayenda
Asemphana bwanji English
Asephana bwanji chichewa munthu waku canada
ππππ kmtu anthu ena ndosaziwikaso bwanji π
ππππ kmtu anthu ena ndosaziwikaso bwanji π
What goes around comes around basitu simple as ABC
Asemphana bwanj chichewa anthu oyankhula chizunguπ
Asemphana bwanj chichewa anthu oyankhula chizunguπ
Anasemphana chiyao
Very bad
Zosayendatu pamenepa π
timati atasephana chizungu kkkkk achila koma!!!
Alipo kd ??? π π π
Anasemphana chichewa achina Tory Lanez π€£π€£π€£
Oimba enawa ndiosadziwikatu
Amusiye bc cz walangidwa kare
Qk recovery
Mmmmm mbola tu nakoso ku malawi kuno tizitelotu apa
Asemphan bwanji chichewa
So badly
Anasemphana chitumbuka
Apa palinkhanitu fuso nkumati akayidi-wo zidazo anazitenga kt Mmmmmm
Koma zovuta ndithu!!
Ubwenzi ongogonana et akaz akuno sangalore azifuna makobili being a boyfriend is very expensive than being a husband in malawi
asemphana bwanji Chichewa munthu oti amayankhula english
πππππ Kma ndaseka, adasemphana chichewa etii?? π
Makosana mwati anasemphana chichewa?ππ
Nde mwati anamuweluza kut akhalako zaka zingat
Ndiye anasephana chichewa
Mukunama
Very sadπ
Asephana chani chichewa kapena chiyawo π
Ok chabwino
They want to kill my superstar...... Koma mikozi mpaka anasephana Chichewa
Anasemphana chizungu
Asemphana cha πππ
Amakaniza thako?
Asemphana chichiwa bwanji ngati nda Malawi
Choipa chisata mwini
Anasephana chizungu π€£π
Ulibhoi Akufuna kutiphera mfana wabho makape amenewa
Mbola
mmmm anasephana zochita not chichewa awa2 nd akunja salakhula chisena chanuchi π€£π€£π€£
Mmmmm ndye zosakhala bhoot
Eeeh so sad π«
Zochita kunja nzovuta bola kwathu komkuno
Zosayendatu π