Pope emwe wasankhidwa uja wakana kuti sakufuna azilandira salary
Pope Leo XIV emwe tsopano padakali pano ndi papa kutsatira kumwalira kwa pope Francis zikumveka kuti wakana kuti sakufuna azilandira Salary m’malo mwake ndalama yomwe inakonzedwa kuti azilandirayo izigwira ntchito zachifundo (Charity works)
Pope Leo XiV wapitiliza kunena kuti pakuti Mpingo wa katolika umampangira chinachilichonse kale monga kumpatsa chakudya, zovala, chitetezo ndi chilichonse chomwe angafune ndiye sizoona kuti azilandiraso salary chifukwa azisowa chochita nayo Kulibwino ndalama zimenezo mwezi uliwonse zizithandizira anthu ena ovutika
Anthu ambiri omwe amva za nkhaniyi maka akhilistu a ku Africa ayamikira chiganizo cha Pope watsopanoyi Ndipo akuti ndipemphero lawo zinthu ngati zomwezi ma pastor ndi a otsogolera ena atengelepo phunziro
Nice one
God bless him
Kod Makosana popangra react choseka ndi pati fukwatu anthu macommentiwa ayamba kuzilowesa kwa chakwera😂😂😂😂
Ndiwaumunthu Mulungu amudalise
Khani ya bwino zimafunika chakwera atengerepo phuziro
❤️❤️❤️🙌
Nkhani yabwino, chofunika ndikuonetsetsa kuti ndalamazo zidzipita koyenerera ko
Maganizo abwno
That’s nice
He's wise we need such people in the world
He's wise we need such people in the world
That is a nice and good decision
That's well
Umunthu
Chakwera atengerepo mphuziro
Umunthu