Malawi vs South Africa? Umu ndi mmene zikuyendela
Mpira umene uli pakati Pa Malawi ndi South Africa uli mkati, ndipo South Africa ikutsogola ndi chigoli Chimodzi kwa duu. Mpira wu ukumenyedwa mu dziko la South Africa relo pa 11 May ku stadium yaku Pretoria yotchedwa Loftus.
Awa ndi masewelo a African Nations championship Qualifiers omwe ma team onse Alipo 48 ndipo anagawidwa muma group 12. Kotelo ma team awili amene atachite bwino mma group stages ndi amene amapambana kukafika ku AFCON. Kotelo masewelo amma group wa ndi Ofunika ndithu.
Tikunena pano Malawi game yawo yambuyo anapambana 1 kwa 0 Kotelo akutaogola ku aggregate koma ndizofunika kuti game ya relolo so Apambane kuti mwayi uchulukilepo.
Peter Mponda anayankhulapo game isanati kuti Cholinga chawo angofuna strategy imene aiganiza yakamenyedwa ka mpira ikatheke, ndiye tiyeni tionele limodzi kuti ma plan amanena wo awaoneka Pamapeto a game yi.
Apa ma team onsewa ali ku half time, tiyeni tidikile chigawo chomalidza
Source : Football Association of Malawi