Article
Kodi lero twine ndi iti?

Kodi lero twine ndi iti?

Ma player a Real Madrid akuti coach ndi amene salibwino, ndiye game yawo relo ndi Barcelona tiyembekedzele kuti awina?

Lero kuli game ya Real Madrid ndi Barcelona FC nthawi 4:15 PM koma nkhani yomwe yakula ndi ya coach wa Real Madrid amene ma player ake anamudandaula kuti salibwino pa game yomwe analuza ndi team ya Arsenal mu league ya Champions league.

Anthu ambiri sanayembekedzele kuti Real Madrid ndi kugonja ndithu ndi team ya Arsenal, koma zitachitika ma player ngati Vinius jnr komanso Mbappe anadandaula kuti ndi vuto la coach wawo 'Carlo Ancelotti' kuti sanapase plan yabwino.

Coach yu zikumveka kuti akupumisidwa ntchito ndipo Real Madrid ikuyembekezera 'Alonso' kukhala coach wa tsopano (zatsimikiza). Koma game yomwe ilipo lero pakati pa Madrid ndi Barcelona coach wake akhala ali yemweyu, ndiye funso lagona pokuti anthu a Real Madrid adalire kapena avomeleze kuti aluza kale kutengela kuti ma player akuti coach salibwino?

Matimuwa ali ndi mbiri limodzi, ndipo awa amakhala masewelo akulu ku league yaku Spain. Real Madrid ndi imene ikusogola pa masewelo onse amene inasewelapo inawina ma game 105, pamene Barcelona inawina masewelo okwana 103 ndipo ma draw alipo okwana 52. Kutengela mbili imeneyi Mukuona kuti team yomwe ingapambane ndi iti lero?

Mongokumbutsana coach wa Madrid yu zikumveka kuti akachoka ku Real Madrid akupitano kukakhala coach wa Brazil national team, ndipo tikunena pano ali ndi dzaka zokwana 65. Kwao kweni kweni ndiku Spain, ndipo team ya Real Madrid wasewela nayo ma game okwana 350 kuphatikiza yomwe ikumenyedwa leroyi . Ulemu wake kwa coach yu, zambili tingodikila game yo mma 4 mu

Admin Jeffrey

Comment Below

upload your music with us to get maximum reach out!