Trump wayankhulapo kale zokhuza Papa wasankhidwa yi, Akuti akudikila kuti awili WA akumane.
PA kuti Papa yu ndi waku America ambili anadziwa kuti Trump akangoidziwa pavuta. Ndipo wayankhuladi pa samba lake la mchezo komanso page ya white house.
Chachikulu akungomufunila ZAbwino papa wasankhidwa yo komanso akuti iye akudikila tsiku limene awili WA atazakumane. ZIkuoneka kuti nkhani a Trump asangalala nayo kwambili.
Uthenga umene alemba a Trump uli mu chingelezi chotele " Congratulations to Cardinal Robert Francis Prevost, who was just named Pope. It is such an honor to realize that he is the first American Pope. What excitement, and what a Great Honor for our Country. I look forward to meeting Pope Leo XIV. It will be a very meaningful moment!"
Congrats
Komatu uyuyu penapake 😂😂😂
Akanakhaladi papa iyeyu koma 😄😄
Trump sazathekadi aaah 🤣🤣🙌 abwere ku malawi kuno uyu Ali ndi khalidwe lachisena 😂😒